Sitidawachotse ndife a Mutharika muchisankho cha 2020-HRDC yatsutsa kwa mtuwagalu
By Chisomo Phiri Limodzi mwa mabungwe akuluakulu omenyera maufulu awanthu mdziko muno la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) latsutsa kwa mtuwagalu zomwe wanena mtsogoleri wa chipani chakale cholamula cha Democratic…