Chakwera wakonzeka kulamulanso mpaka 2030
Mtsogoleli wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati pamene a Malawi ambili akhala akuona zitukuko zomwe iye akupanga kuphatikizapo kubwezeretsanso ntchito za njanji zomwe zinafa zaka 20 zapitazo, ndichosadwabwitsanso kuti mamembala a kuchipani anamukhulupila kumusakhanso pa udindo.