Nduna ya zamdziko Dr Ken Zikhale Ng’oma ilikimbikitsa akaidi kuti akalembetse mkaundula wa ma voti
Wolemba Linda Kwanjana Dr Zikhale Ng’oma yemwe ndi nduna yowona nkhani za chitetezo chamdziko a lero inakayendera Ndende ya Maula mumzinda wa Lilongwe. Mukulankhula kwawo, ndunayi inapempha akaidi okhala mndende…